Song Cover Image

Mwanisiya Mumdima

V6-MINI

MUNANDISYA MUMDIMA (You Left Me In The Dark) Mwanisiya mumdima, mwanisiya mumdima (Male voice) Munali kunikonda, nanga bwanji mwanisiya? (Both) Mwanisiya mumdima, mtima wanga ukulira (Female voice)[Hook] Mwanisiya mumdima, nili alone in this house [Verse 1] reyce...! Nauka m'mawa, sinikuwona nkhope yanu (Male voice) Pafoni yanu simukuyankha, mtima wanga ukumva kuwawa (Male voice) Nimakumbukira ma promise, munanena kuti muzachita (Female voice) Koma lelo mwapita, mwanisiya na ka boy wina (Female voice) Mwanisiya mumdima, moyo wanga wasila (Both) Mwanisiya mumdima, misozi yanga sikutha (Both - harmony)[Chorus] Mwanisiya mumdima, bwanji munachita chonchi? [Verse 2] Banja lonse likunifunsa, bwanji simuseka? (Male voice) Nimati nilibwino, koma mkati nikulira (Male voice) Chikondi chomwe ninakupatsani, sichinali chamasobela (Female voice) Koma mwandipweteka, mtima wanga wathyoka (Both - painful) [Bridge - Slow] Ngati mubwerera, mtima wanga uli pano (Female voice - soft) Koma ngati simubwera, ja akuona (Male voice - soft) Chikondi ni ululu, ndaphunzira lelo (Both) [Final Hook - Powerful, All voices] Mwanisiya mumdima, mwanisiya mumdima (Both) Mudatenga mtima wanga, mwapita nawo kutali (Both) Mwanisiya mumdima, sinizakukondansoni (Male voice crying) Mwanisiya mumdima... Zikomo (Female voice whisper) --- KING REYCE RECORDINGS From Lusaka to the world One.. Family... One lebal... One.. Vision